Yobu 28:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Ndiyeno anauza munthu kuti: ‘Tamvera, kuopa Yehova ndi nzeru,+Ndipo kupewa zoipa ndiko kumvetsa zinthu.’”+ Miyambo 8:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Kuopa Yehova kumatanthauza kudana ndi zoipa.+ Ndimadana ndi kudzikweza, kunyada,+ njira yoipa ndiponso mawu achinyengo.+ Yeremiya 32:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Ndidzachita nawo pangano+ lomwe lidzakhalapo mpaka kalekale. Panganoli lidzakhala lakuti sindidzasiya kuwachitira zinthu zabwino+ ndipo ndidzawapatsa mtima woti azindiopa kuti asachoke kwa ine.+
28 Ndiyeno anauza munthu kuti: ‘Tamvera, kuopa Yehova ndi nzeru,+Ndipo kupewa zoipa ndiko kumvetsa zinthu.’”+
13 Kuopa Yehova kumatanthauza kudana ndi zoipa.+ Ndimadana ndi kudzikweza, kunyada,+ njira yoipa ndiponso mawu achinyengo.+
40 Ndidzachita nawo pangano+ lomwe lidzakhalapo mpaka kalekale. Panganoli lidzakhala lakuti sindidzasiya kuwachitira zinthu zabwino+ ndipo ndidzawapatsa mtima woti azindiopa kuti asachoke kwa ine.+