Salimo 146:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Yehova akuteteza alendo amene akukhala mʼdziko la eni.Amathandiza mwana wamasiye komanso mkazi wamasiye.+Koma amasokoneza mapulani a anthu oipa.*+
9 Yehova akuteteza alendo amene akukhala mʼdziko la eni.Amathandiza mwana wamasiye komanso mkazi wamasiye.+Koma amasokoneza mapulani a anthu oipa.*+