-
Levitiko 26:21Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
21 Koma mukapitirizabe kuchita zosemphana ndi zofuna zanga, osafuna kundimvera, ndidzakulangani kuchulukitsa maulendo 7 mogwirizana ndi machimo anu.
-
-
Miyambo 1:32Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
32 Chifukwa kupanduka kwa anthu osadziwa zinthu kudzawaphetsa,
Ndipo mphwayi za anthu opusa zidzawawonongetsa.
-