Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Machitidwe 16:23-25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Atawakwapula zikoti zambiri, anawatsekera mʼndende ndi kulamula woyangʼanira ndende kuti aziwalondera nʼcholinga choti asathawe.+ 24 Popeza kuti anamulamula zimenezi, iye anakawaika mʼchipinda chamkati cha ndendeyo nʼkumanga mapazi awo mʼmatangadza.

      25 Koma chapakati pa usiku, Paulo ndi Sila anayamba kupemphera ndiponso kutamanda Mulungu poimba nyimbo,+ moti akaidi ena ankawamva.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena