Salimo 41:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Koma ine mumandithandiza chifukwa choti ndine wokhulupirika,+Ndipo mudzasangalala nane mpaka kalekale.*+ Miyambo 28:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Amene amayenda mosalakwitsa kanthu adzapulumutsidwa,+Koma amene njira zake ndi zokhotakhota adzagwa mwadzidzidzi.+
12 Koma ine mumandithandiza chifukwa choti ndine wokhulupirika,+Ndipo mudzasangalala nane mpaka kalekale.*+
18 Amene amayenda mosalakwitsa kanthu adzapulumutsidwa,+Koma amene njira zake ndi zokhotakhota adzagwa mwadzidzidzi.+