Miyambo 8:35, 36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Chifukwa wondipeza ine adzapeza moyo,+Ndipo Yehova amasangalala naye. 36 Koma amene amandinyalanyaza amadzipweteka yekha,Ndipo amene amadana ndi ine amakonda imfa.”+
35 Chifukwa wondipeza ine adzapeza moyo,+Ndipo Yehova amasangalala naye. 36 Koma amene amandinyalanyaza amadzipweteka yekha,Ndipo amene amadana ndi ine amakonda imfa.”+