Miyambo 6:16, 17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Pali zinthu 6 zimene Yehova amadana nazo.Zilipo zinthu 7 zimene amanyansidwa nazo: 17 Maso odzikweza,+ lilime lonama,+ manja amene amakhetsa magazi a anthu osalakwa,+ Miyambo 8:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Kuopa Yehova kumatanthauza kudana ndi zoipa.+ Ndimadana ndi kudzikweza, kunyada,+ njira yoipa ndiponso mawu achinyengo.+ Miyambo 21:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Maso odzikweza komanso mtima wonyadaZili ngati nyale imene imatsogolera anthu oipa, koma zimenezi ndi tchimo.+
16 Pali zinthu 6 zimene Yehova amadana nazo.Zilipo zinthu 7 zimene amanyansidwa nazo: 17 Maso odzikweza,+ lilime lonama,+ manja amene amakhetsa magazi a anthu osalakwa,+ Miyambo 8:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Kuopa Yehova kumatanthauza kudana ndi zoipa.+ Ndimadana ndi kudzikweza, kunyada,+ njira yoipa ndiponso mawu achinyengo.+ Miyambo 21:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Maso odzikweza komanso mtima wonyadaZili ngati nyale imene imatsogolera anthu oipa, koma zimenezi ndi tchimo.+
13 Kuopa Yehova kumatanthauza kudana ndi zoipa.+ Ndimadana ndi kudzikweza, kunyada,+ njira yoipa ndiponso mawu achinyengo.+
4 Maso odzikweza komanso mtima wonyadaZili ngati nyale imene imatsogolera anthu oipa, koma zimenezi ndi tchimo.+