Luka 4:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Zitatero onse anayamba kumutamanda komanso anadabwa ndi mawu ogwira mtima amene anatuluka pakamwa pake,+ moti ankanena kuti: “Kodi si mwana wa Yosefe ameneyu?”+ Akolose 4:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Nthawi zonse mawu anu azisonyeza kuti ndinu okoma mtima ndipo azikhala okoma ngati kuti mwawathira mchere,+ kuti mudziwe mmene mungayankhire munthu aliyense.+
22 Zitatero onse anayamba kumutamanda komanso anadabwa ndi mawu ogwira mtima amene anatuluka pakamwa pake,+ moti ankanena kuti: “Kodi si mwana wa Yosefe ameneyu?”+
6 Nthawi zonse mawu anu azisonyeza kuti ndinu okoma mtima ndipo azikhala okoma ngati kuti mwawathira mchere,+ kuti mudziwe mmene mungayankhire munthu aliyense.+