Miyambo 10:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pakamwa pa wolungama pamachokera moyo,+Koma pakamwa pa anthu oipa pamabisa zachiwawa.+