Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 23:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Ndiyeno Davide anafunsira kwa Yehova+ kuti: “Kodi ndipite kukapha Afilisiti?” Yehova anayankha Davide kuti: “Pita, ukaphe Afilisitiwo ndipo ukapulumutse Keila.”

  • 1 Samueli 23:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Choncho Davide anafunsiranso kwa Yehova.+ Ndipo Yehova anamuyankha kuti: “Nyamuka, pita ku Keila, chifukwa ndipereka Afilisitiwo mʼmanja mwako.”+

  • Nehemiya 1:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Inu Yehova, chonde mvetserani pemphero la ine mtumiki wanu ndiponso pemphero la atumiki anu amene amaopa dzina lanu ndi mtima wonse. Chonde, ndithandizeni ine mtumiki wanu kuti zinthu zindiyendere bwino lero ndipo munthuyu andichitire chifundo.”+

      Pa nthawiyi ndinali woperekera zakumwa kwa mfumu.+

  • Afilipi 4:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Musamade nkhawa ndi chinthu chilichonse.+ Mʼmalomwake, nthawi zonse muzipemphera kwa Mulungu, muzimuchonderera kuti azikutsogolerani pa chilichonse ndipo nthawi zonse muzimuthokoza.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena