Yobu 28:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Sizingagulidwe ndi golide woyenga bwino,Ndipo munthu sangapereke siliva kuti apeze nzeru.+ Yobu 28:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Miyala yamtengo wapatali ya korali ndi kulusitalo sitingaiyerekezere nʼkomwe ndi nzeru.+Ndipo thumba lodzaza ndi nzeru ndi lamtengo wapatali kuposa thumba lodzaza ndi ngale.
18 Miyala yamtengo wapatali ya korali ndi kulusitalo sitingaiyerekezere nʼkomwe ndi nzeru.+Ndipo thumba lodzaza ndi nzeru ndi lamtengo wapatali kuposa thumba lodzaza ndi ngale.