Salimo 141:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Wolungama akandimenya ndiye kuti wandisonyeza chikondi chokhulupirika.+Akandidzudzula zingakhale ngati wandidzoza mafuta pamutu,+Mafuta amene mutu wanga sungawakane.+ Ndidzapemphererabe anthu olungama ngakhale pamene masoka awagwera. Miyambo 1:8, 9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Mwana wanga, uzimvera malangizo a bambo ako,+Ndipo usasiye kutsatira malangizo* a mayi ako.+ 9 Malangizowa ali ngati nkhata ya maluwa yokongola pamutu pako+Komanso mkanda wokongola mʼkhosi mwako.+ Miyambo 9:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Usadzudzule wonyoza chifukwa angadane nawe.+ Dzudzula munthu wanzeru ndipo adzakukonda.+
5 Wolungama akandimenya ndiye kuti wandisonyeza chikondi chokhulupirika.+Akandidzudzula zingakhale ngati wandidzoza mafuta pamutu,+Mafuta amene mutu wanga sungawakane.+ Ndidzapemphererabe anthu olungama ngakhale pamene masoka awagwera.
8 Mwana wanga, uzimvera malangizo a bambo ako,+Ndipo usasiye kutsatira malangizo* a mayi ako.+ 9 Malangizowa ali ngati nkhata ya maluwa yokongola pamutu pako+Komanso mkanda wokongola mʼkhosi mwako.+