Salimo 104:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ntchito zanu ndi zochuluka, inu Yehova!+ Zonsezo munazipanga mwanzeru.+ Dziko lapansi ladzaza ndi zinthu zimene munapanga.
24 Ntchito zanu ndi zochuluka, inu Yehova!+ Zonsezo munazipanga mwanzeru.+ Dziko lapansi ladzaza ndi zinthu zimene munapanga.