1 Samueli 25:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Chonde mbuyanga, musaganizire za Nabala, munthu wopanda pake,+ chifukwa zochita zake nʼzogwirizana ndi dzina lake. Dzina lake ndi Nabala* ndipo ndi wopandadi nzeru. Koma ine kapolo wanu sindinawaone anyamata amene inu mbuyanga munawatuma.
25 Chonde mbuyanga, musaganizire za Nabala, munthu wopanda pake,+ chifukwa zochita zake nʼzogwirizana ndi dzina lake. Dzina lake ndi Nabala* ndipo ndi wopandadi nzeru. Koma ine kapolo wanu sindinawaone anyamata amene inu mbuyanga munawatuma.