2 Samueli 12:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndiyeno Natani anauza Davide kuti: “Munthu ameneyu ndi iweyo. Yehova Mulungu wa Isiraeli wanena kuti, ‘Ndinakudzoza kuti ukhale mfumu ya Isiraeli+ ndipo ndinakupulumutsa mʼmanja mwa Sauli.+ 2 Samueli 12:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Nʼchifukwa chiyani unanyoza mawu a Yehova pochita zoipa pamaso pake? Unapha Uriya Muhiti ndi lupanga.+ Kenako unatenga mkazi wake kuti akhale mkazi wako+ utapha Uriyayo ndi lupanga la Aamoni.+ Salimo 141:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Wolungama akandimenya ndiye kuti wandisonyeza chikondi chokhulupirika.+Akandidzudzula zingakhale ngati wandidzoza mafuta pamutu,+Mafuta amene mutu wanga sungawakane.+ Ndidzapemphererabe anthu olungama ngakhale pamene masoka awagwera. Chivumbulutso 3:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Onse amene ndimawakonda, ndimawadzudzula komanso kuwalanga.+ Choncho khala wodzipereka ndipo ulape.+
7 Ndiyeno Natani anauza Davide kuti: “Munthu ameneyu ndi iweyo. Yehova Mulungu wa Isiraeli wanena kuti, ‘Ndinakudzoza kuti ukhale mfumu ya Isiraeli+ ndipo ndinakupulumutsa mʼmanja mwa Sauli.+
9 Nʼchifukwa chiyani unanyoza mawu a Yehova pochita zoipa pamaso pake? Unapha Uriya Muhiti ndi lupanga.+ Kenako unatenga mkazi wake kuti akhale mkazi wako+ utapha Uriyayo ndi lupanga la Aamoni.+
5 Wolungama akandimenya ndiye kuti wandisonyeza chikondi chokhulupirika.+Akandidzudzula zingakhale ngati wandidzoza mafuta pamutu,+Mafuta amene mutu wanga sungawakane.+ Ndidzapemphererabe anthu olungama ngakhale pamene masoka awagwera.
19 Onse amene ndimawakonda, ndimawadzudzula komanso kuwalanga.+ Choncho khala wodzipereka ndipo ulape.+