1 Samueli 23:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Kenako Yonatani mwana wa Sauli anapita kwa Davide ku Horesi ndipo anamuthandiza* kuti apeze mphamvu kuchokera kwa Yehova.+ Miyambo 15:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Munthu amasangalala akapereka yankho labwino,*+Ndipo mawu onenedwa pa nthawi yoyenera ndi abwino kwambiri.+ Miyambo 16:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Mawu okoma ali ngati chisa cha uchi.Amakhala okoma kwa munthu ndipo amachiritsa mafupa.+
16 Kenako Yonatani mwana wa Sauli anapita kwa Davide ku Horesi ndipo anamuthandiza* kuti apeze mphamvu kuchokera kwa Yehova.+
23 Munthu amasangalala akapereka yankho labwino,*+Ndipo mawu onenedwa pa nthawi yoyenera ndi abwino kwambiri.+