Miyambo 20:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ngati munthu walonjeza kuti akhala chikole kwa mlendo, umulande chovala chake.+Komanso umulande chikole ngati walonjeza zimenezi kwa mkazi wachilendo.+
16 Ngati munthu walonjeza kuti akhala chikole kwa mlendo, umulande chovala chake.+Komanso umulande chikole ngati walonjeza zimenezi kwa mkazi wachilendo.+