Miyambo 23:4, 5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Usadzitopetse pofuna kupeza chuma.+ Leka kuchita zimenezi, mʼmalomwake uzisonyeza kuti ndiwe womvetsa zinthu.* 5 Ukayangʼana pamene panali chumacho, umapeza kuti palibe,+Chifukwa ndithu chimamera mapiko ngati chiwombankhanga nʼkuulukira mʼmwamba.+ 1 Timoteyo 6:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ulangize* anthu achuma mʼdzikoli* kuti asakhale odzikweza, ndiponso kuti asamadalire chuma chosadalirika,+ koma azidalira Mulungu, amene amatipatsa mowolowa manja zinthu zonse zomwe timasangalala nazo.+
4 Usadzitopetse pofuna kupeza chuma.+ Leka kuchita zimenezi, mʼmalomwake uzisonyeza kuti ndiwe womvetsa zinthu.* 5 Ukayangʼana pamene panali chumacho, umapeza kuti palibe,+Chifukwa ndithu chimamera mapiko ngati chiwombankhanga nʼkuulukira mʼmwamba.+
17 Ulangize* anthu achuma mʼdzikoli* kuti asakhale odzikweza, ndiponso kuti asamadalire chuma chosadalirika,+ koma azidalira Mulungu, amene amatipatsa mowolowa manja zinthu zonse zomwe timasangalala nazo.+