Miyambo 14:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Amene amabera munthu wosauka mwachinyengo amanyoza amene anamupanga,+Koma amene amakomera mtima munthu wosauka amalemekeza amene anamupanga.+
31 Amene amabera munthu wosauka mwachinyengo amanyoza amene anamupanga,+Koma amene amakomera mtima munthu wosauka amalemekeza amene anamupanga.+