Miyambo 16:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndi bwino kukhala ndi zinthu zochepa koma uli wachilungamo+Kusiyana nʼkupeza zinthu zambiri mopanda chilungamo.+ Miyambo 19:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ndi bwino kukhala wosauka nʼkumachita zinthu mokhulupirika+Kusiyana nʼkukhala munthu wopusa nʼkumalankhula mabodza.+
8 Ndi bwino kukhala ndi zinthu zochepa koma uli wachilungamo+Kusiyana nʼkupeza zinthu zambiri mopanda chilungamo.+
19 Ndi bwino kukhala wosauka nʼkumachita zinthu mokhulupirika+Kusiyana nʼkukhala munthu wopusa nʼkumalankhula mabodza.+