Miyambo 23:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Usakhale mʼgulu la anthu amene amamwa vinyo wambiri.+Usakhale mʼgulu la anthu amene amadya nyama mosusuka,+ 1 Akorinto 15:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Musapusitsidwe.* Kugwirizana ndi anthu oipa kumawononga makhalidwe abwino.+
20 Usakhale mʼgulu la anthu amene amamwa vinyo wambiri.+Usakhale mʼgulu la anthu amene amadya nyama mosusuka,+ 1 Akorinto 15:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Musapusitsidwe.* Kugwirizana ndi anthu oipa kumawononga makhalidwe abwino.+