Esitere 8:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Mʼzigawo zonse ndiponso mʼmizinda yonse kumene lamulo la mfumu linafika, Ayuda ankasangalala, kukondwera ndiponso kuchita phwando komanso zikondwerero. Anthu ambiri amʼdzikomo anayamba kunena kuti ndi Ayuda+ chifukwa ankaopa kwambiri Ayudawo.
17 Mʼzigawo zonse ndiponso mʼmizinda yonse kumene lamulo la mfumu linafika, Ayuda ankasangalala, kukondwera ndiponso kuchita phwando komanso zikondwerero. Anthu ambiri amʼdzikomo anayamba kunena kuti ndi Ayuda+ chifukwa ankaopa kwambiri Ayudawo.