Miyambo 15:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Munthu wosachedwa kupsa mtima amayambitsa mkangano,+Koma munthu amene sakwiya msanga amaziziritsa mkangano.+
18 Munthu wosachedwa kupsa mtima amayambitsa mkangano,+Koma munthu amene sakwiya msanga amaziziritsa mkangano.+