-
Esitere 6:10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Nthawi yomweyo mfumu inauza Hamani kuti: “Fulumira, tenga chovala ndi hatchi ngati mmene wanenera, ndipo ukachitire zimenezi Moredikayi, Myuda, amene ali kugeti. Uonetsetse kuti wachita zonse zimene wanenazi.”
-