Aroma 12:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ngati nʼkotheka, yesetsani mmene mungathere kuti muzikhala mwamtendere ndi anthu onse.+