Miyambo 6:16, 17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Pali zinthu 6 zimene Yehova amadana nazo.Zilipo zinthu 7 zimene amanyansidwa nazo: 17 Maso odzikweza,+ lilime lonama,+ manja amene amakhetsa magazi a anthu osalakwa,+
16 Pali zinthu 6 zimene Yehova amadana nazo.Zilipo zinthu 7 zimene amanyansidwa nazo: 17 Maso odzikweza,+ lilime lonama,+ manja amene amakhetsa magazi a anthu osalakwa,+