Oweruza 11:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Atangomuona, anangʼamba zovala zake nʼkunena kuti: “Mayine mwana wanga! Ndikumva chisoni kwambiri chifukwa ndikukuchotsa pakhomo. Ndalonjeza kwa Yehova ndipo sindingathe kubweza mawu anga.”+
35 Atangomuona, anangʼamba zovala zake nʼkunena kuti: “Mayine mwana wanga! Ndikumva chisoni kwambiri chifukwa ndikukuchotsa pakhomo. Ndalonjeza kwa Yehova ndipo sindingathe kubweza mawu anga.”+