Miyambo 23:4, 5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Usadzitopetse pofuna kupeza chuma.+ Leka kuchita zimenezi, mʼmalomwake uzisonyeza kuti ndiwe womvetsa zinthu.* 5 Ukayangʼana pamene panali chumacho, umapeza kuti palibe,+Chifukwa ndithu chimamera mapiko ngati chiwombankhanga nʼkuulukira mʼmwamba.+ Mateyu 6:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Siyani kudziunjikira chuma padziko lapansi,+ pomwe njenjete* komanso dzimbiri zimawononga ndiponso pomwe akuba amathyola nʼkuba.
4 Usadzitopetse pofuna kupeza chuma.+ Leka kuchita zimenezi, mʼmalomwake uzisonyeza kuti ndiwe womvetsa zinthu.* 5 Ukayangʼana pamene panali chumacho, umapeza kuti palibe,+Chifukwa ndithu chimamera mapiko ngati chiwombankhanga nʼkuulukira mʼmwamba.+
19 Siyani kudziunjikira chuma padziko lapansi,+ pomwe njenjete* komanso dzimbiri zimawononga ndiponso pomwe akuba amathyola nʼkuba.