Mlaliki 4:2, 3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndinazindikira kuti anthu amene anafa kale ali bwino kuposa anthu amene ali ndi moyo.+ 3 Koma amene ali bwino kwambiri kuposa onsewa ndi amene sanabadwe,+ amene sanaone zinthu zoipa zimene zikuchitika padziko lapansi pano.+
2 Ndinazindikira kuti anthu amene anafa kale ali bwino kuposa anthu amene ali ndi moyo.+ 3 Koma amene ali bwino kwambiri kuposa onsewa ndi amene sanabadwe,+ amene sanaone zinthu zoipa zimene zikuchitika padziko lapansi pano.+