Yobu 3:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Nʼchifukwa chiyani sindinafe pobadwa? Nʼchifukwa chiyani sindinamwalire nditatuluka mʼmimba?+ Yobu 3:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Chifukwa pano bwenzi ndikugona popanda wondisokoneza.+Bwenzi ndili mʼtulo komanso ndikupuma+ Yobu 14:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 “Munthu wobadwa kwa mkazi,Amakhala ndi moyo waufupi+ komanso wodzaza ndi mavuto.+
13 Chifukwa pano bwenzi ndikugona popanda wondisokoneza.+Bwenzi ndili mʼtulo komanso ndikupuma+ Yobu 14:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 “Munthu wobadwa kwa mkazi,Amakhala ndi moyo waufupi+ komanso wodzaza ndi mavuto.+