2 Samueli 5:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Choncho akulu onse a Isiraeli anabwera kwa mfumu ku Heburoni ndipo Mfumu Davide inachita nawo pangano+ ku Heburoniko pamaso pa Yehova. Kenako iwo anadzoza Davide kuti akhale mfumu ya Isiraeli.+
3 Choncho akulu onse a Isiraeli anabwera kwa mfumu ku Heburoni ndipo Mfumu Davide inachita nawo pangano+ ku Heburoniko pamaso pa Yehova. Kenako iwo anadzoza Davide kuti akhale mfumu ya Isiraeli.+