Salimo 10:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Chifukwa cha kudzikweza, munthu woipa safufuza kuti adziwe Mulungu.Iye amangoganiza kuti: “Kulibe Mulungu.”+ Salimo 10:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Mumtima mwake amanena kuti: “Sindidzagwedezeka.*Ku mibadwomibadwo,Tsoka silidzandigwera.”+
4 Chifukwa cha kudzikweza, munthu woipa safufuza kuti adziwe Mulungu.Iye amangoganiza kuti: “Kulibe Mulungu.”+