-
Salimo 25:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Musakumbukire machimo amene ndinachita ndili mnyamata komanso zolakwa zanga.
-
-
2 Timoteyo 2:22Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
22 Choncho thawa zilakolako za unyamata, koma tsatira chilungamo, chikhulupiriro, chikondi ndi mtendere limodzi ndi anthu oitana pa Ambuye ndi mtima woyera.
-