-
1 Mafumu 10:3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 Solomo anayankha mafunso ake onse. Panalibe chimene mfumuyo inalephera kumufotokozera.
-
-
1 Mafumu 10:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Choncho inauza mfumuyo kuti: “Nkhani zimene ndinamva kudziko langa zokhudza zimene mwakwanitsa kuchita komanso nzeru zanu ndi zoona.
-