Nyimbo ya Solomo 1:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Undikise ndi milomo yako,Chifukwa chikondi chimene umandisonyeza chimaposa vinyo.+ Nyimbo ya Solomo 4:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Chikondi chimene umandisonyeza nʼchokoma,+ iwe mchemwali wanga, mkwatibwi wanga. Chikondi chimene umandisonyeza nʼchabwino kuposa vinyo,+Ndipo kununkhira kwa mafuta ako odzola nʼkoposa zonunkhira zamitundu yonse.+
10 Chikondi chimene umandisonyeza nʼchokoma,+ iwe mchemwali wanga, mkwatibwi wanga. Chikondi chimene umandisonyeza nʼchabwino kuposa vinyo,+Ndipo kununkhira kwa mafuta ako odzola nʼkoposa zonunkhira zamitundu yonse.+