-
Nyimbo ya Solomo 4:16Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 Dzuka, iwe mphepo yakumpoto.
Bwera, iwe mphepo yakumʼmwera.
Womba pamunda wanga.
Kununkhira kwake kufalikire.”
“Wachikondi wanga alowe mʼmunda wake
Kuti adzadye zipatso zake zabwino kwambiri.”
-