Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yoswa 15:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Ichi chinali cholowa cha fuko la Yuda, motsatira mabanja awo.

  • Yoswa 15:62
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 62 Nibisani, Mzinda wa Mchere ndi Eni-gedi.+ Mizinda 6 ndi midzi yake.

  • 1 Samueli 23:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 Ndiyeno Davide anachoka kumeneko nʼkukakhala kumalo ovuta kufikako a ku Eni-gedi.+

  • 2 Mbiri 20:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Choncho anthu anapita kukauza Yehosafati kuti: “Kwabwera chigulu cha anthu kuchokera kuchigawo chakunyanja,* ku Edomu,+ kudzamenyana nanu ndipo ali ku Hazazoni-tamara, kapena kuti ku Eni-gedi.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena