-
1 Samueli 30:11, 12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Ndiyeno anapeza munthu wina wa ku Iguputo patchire. Anamutenga nʼkupita naye kwa Davide ndipo anamupatsa chakudya ndi madzi akumwa. 12 Anamupatsanso keke ya nkhuyu zouma ndi makeke awiri a mphesa zouma. Atadya anapeza mphamvu, chifukwa anakhala osadya chakudya kapena kumwa madzi kwa masiku atatu, masana ndi usiku.
-