Yeremiya 8:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ngakhale dokowe, mbalame youluka mumlengalenga, imadziwa bwino nthawi yake yoikidwiratu.Ndipo njiwa, namzeze komanso mbalame zina, zimadziwa nthawi yobwerera kumene zachokera.* Koma anthu anga sakudziwa chiweruzo cha Yehova.”’+
7 Ngakhale dokowe, mbalame youluka mumlengalenga, imadziwa bwino nthawi yake yoikidwiratu.Ndipo njiwa, namzeze komanso mbalame zina, zimadziwa nthawi yobwerera kumene zachokera.* Koma anthu anga sakudziwa chiweruzo cha Yehova.”’+