2 Samueli 12:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ndiyeno Davide anatonthoza mkazi wake Bati-seba.+ Kenako anagona naye ndipo patapita nthawi, anabereka mwana wamwamuna yemwe anamupatsa dzina lakuti Solomo.*+ Yehova anamʼkonda mwana ameneyu,+ Miyambo 4:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndinali mwana wabwino kwambiri kwa bambo anga+Ndipo mayi anga ankandikonda kwambiri.+
24 Ndiyeno Davide anatonthoza mkazi wake Bati-seba.+ Kenako anagona naye ndipo patapita nthawi, anabereka mwana wamwamuna yemwe anamupatsa dzina lakuti Solomo.*+ Yehova anamʼkonda mwana ameneyu,+