-
Nyimbo ya Solomo 4:13, 14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Uli ngati munda* wa mitengo imene nthambi zake zili ndi makangaza ambiri
Umene uli ndi zipatso zabwino kwambiri, maluwa a hena ndi mitengo ya nado,
14 Nado,+ maluwa a safironi, mabango onunkhira,+ sinamoni,+
Komanso mitengo yosiyanasiyana ya lubani, mule, aloye,+
Ndi zonunkhira zonse zabwino kwambiri.+
-