Nyimbo ya Solomo 4:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Milomo yako imakha uchi wapachisa,+ iwe mkwatibwi wanga. Uchi ndi mkaka zili kuseri kwa lilime lako,+Ndipo kafungo konunkhira ka zovala zako kakumveka ngati kafungo konunkhira ka ku Lebanoni.
11 Milomo yako imakha uchi wapachisa,+ iwe mkwatibwi wanga. Uchi ndi mkaka zili kuseri kwa lilime lako,+Ndipo kafungo konunkhira ka zovala zako kakumveka ngati kafungo konunkhira ka ku Lebanoni.