-
Luka 2:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Mʼdera limeneli munalinso abusa amene ankagonera kumalo odyetsera ziweto nʼkumayangʼanira nkhosa zawo usiku wonse.