Nyimbo ya Solomo 1:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 “Ndiwe wokongola wokondedwa wanga. Ndiwe chiphadzuwa. Maso ako ali ngati maso a njiwa.”+ Nyimbo ya Solomo 4:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Watenga mtima wanga,+ iwe mchemwali wanga, mkwatibwi wanga,Watenga mtima wanga utangondiyangʼana kamodzi kokha,Ndiponso ndi mkanda wa mʼkhosi mwako. Nyimbo ya Solomo 7:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Khosi lako+ lili ngati nsanja ya mnyanga wa njovu.+ Maso ako+ ali ngati madamu a madzi a ku Hesiboni,+Amene ali pafupi ndi geti la Bati-rabimu. Mphuno yako ili ngati nsanja ya ku Lebanoni,Imene inayangʼana cha ku Damasiko.
9 Watenga mtima wanga,+ iwe mchemwali wanga, mkwatibwi wanga,Watenga mtima wanga utangondiyangʼana kamodzi kokha,Ndiponso ndi mkanda wa mʼkhosi mwako.
4 Khosi lako+ lili ngati nsanja ya mnyanga wa njovu.+ Maso ako+ ali ngati madamu a madzi a ku Hesiboni,+Amene ali pafupi ndi geti la Bati-rabimu. Mphuno yako ili ngati nsanja ya ku Lebanoni,Imene inayangʼana cha ku Damasiko.