Danieli 9:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Aisiraeli onse aphwanya Chilamulo chanu ndipo apatuka posamvera mawu anu. Choncho inu mwatitsanulira temberero ndi malumbiro amene analembedwa mʼChilamulo cha Mose, mtumiki wanu,+ chifukwa takuchimwirani.
11 Aisiraeli onse aphwanya Chilamulo chanu ndipo apatuka posamvera mawu anu. Choncho inu mwatitsanulira temberero ndi malumbiro amene analembedwa mʼChilamulo cha Mose, mtumiki wanu,+ chifukwa takuchimwirani.