Ekisodo 38:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Kenako anapanga beseni losambira lakopa+ ndi choikapo chake chakopa. Popanga zimenezi anagwiritsa ntchito magalasi odziyangʼanira* a azimayi amene ankatumikira pakhomo la chihema chokumanako.
8 Kenako anapanga beseni losambira lakopa+ ndi choikapo chake chakopa. Popanga zimenezi anagwiritsa ntchito magalasi odziyangʼanira* a azimayi amene ankatumikira pakhomo la chihema chokumanako.