Salimo 89:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Mkono wanu ndi wamphamvu,+Dzanja lanu ndi lamphamvu,+Dzanja lanu lamanja lapambana.+