Deuteronomo 20:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 “Mukapita kunkhondo kukamenyana ndi adani anu, nʼkuona kuti ali ndi mahatchi, magaleta ankhondo komanso asilikali ochuluka kuposa inu, musachite nawo mantha chifukwa Yehova Mulungu wanu, amene anakutulutsani mʼdziko la Iguputo ali ndi inu.+ Salimo 46:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 Mulungu ndi pothawira pathu komanso mphamvu yathu,+Thandizo lopezeka mosavuta pa nthawi ya mavuto.+ Aroma 8:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Ndiye tinene kuti chiyani pamenepa? Ngati Mulungu ali kumbali yathu, ndani adzatsutsana nafe?+
20 “Mukapita kunkhondo kukamenyana ndi adani anu, nʼkuona kuti ali ndi mahatchi, magaleta ankhondo komanso asilikali ochuluka kuposa inu, musachite nawo mantha chifukwa Yehova Mulungu wanu, amene anakutulutsani mʼdziko la Iguputo ali ndi inu.+
46 Mulungu ndi pothawira pathu komanso mphamvu yathu,+Thandizo lopezeka mosavuta pa nthawi ya mavuto.+