Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 30:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Mulungu adzabweretsa mvula pambewu zanu zimene munadzala munthaka,+ ndipo chakudya chochokera munthakayo chidzakhala chochuluka komanso chopatsa thanzi.*+ Pa tsiku limenelo, ziweto zanu zidzadya msipu pamalo aakulu odyetserapo ziweto.+

  • Yoweli 3:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Nthawi imeneyo mʼmapiri akuluakulu mudzatuluka vinyo wotsekemera.+

      Mʼmapiri angʼonoangʼono mudzayenda mkaka.

      Ndipo mʼmitsinje yonse ya Yuda mudzayenda madzi.

      Kasupe adzatuluka mʼnyumba ya Yehova,+

      Ndipo adzathirira chigwa cha Mitengo ya Mthethe.

  • Zekariya 9:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Ubwino wake ndi waukulu kwambiri,+

      Ndiponso iye ndi wooneka bwino kwambiri.

      Tirigu adzapatsa mphamvu anyamata,

      Ndipo vinyo watsopano adzapatsa mphamvu anamwali.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena