Deuteronomo 31:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Tsopano Yehova anauza Mose kuti: “Iweyo watsala pangʼono kufa,* ndipo anthu awa adzakhala osakhulupirika kwa ine ndipo adzayamba kulambira milungu yachilendo imene ili mʼdziko limene akupita.+ Iwo adzandisiya+ nʼkuphwanya pangano limene ndinapangana nawo.+ Yeremiya 2:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Yehova wanena kuti: “Kodi makolo anu anandipeza ndi vuto lotani+Kuti asochere nʼkupita kutali ndi ine,Nʼkuyamba kutsatira mafano opanda pake,+ iwonso nʼkukhala anthu opanda pake?+
16 Tsopano Yehova anauza Mose kuti: “Iweyo watsala pangʼono kufa,* ndipo anthu awa adzakhala osakhulupirika kwa ine ndipo adzayamba kulambira milungu yachilendo imene ili mʼdziko limene akupita.+ Iwo adzandisiya+ nʼkuphwanya pangano limene ndinapangana nawo.+
5 Yehova wanena kuti: “Kodi makolo anu anandipeza ndi vuto lotani+Kuti asochere nʼkupita kutali ndi ine,Nʼkuyamba kutsatira mafano opanda pake,+ iwonso nʼkukhala anthu opanda pake?+